Masalmo 121:7-8 Buku Lopatulika 1992 (BL92) Yehova adzakusunga kukucotsera zoipa ziri zonse;Adzasunga moyo wako. Yehova adzasungira kuturuka kwako ndi kulowa