Masalmo 121:6-8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

6. Dzuwa silidzawamba usana,Mwezi sudzakupanda usiku.

7. Yehova adzakusunga kukucotsera zoipa ziri zonse;Adzasunga moyo wako.

8. Yehova adzasungira kuturuka kwako ndi kulowa kwako,Kuyambira tsopano kufikira nthawi zonse.

Masalmo 121