Masalmo 121:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92) Ndikweza maso anga kumapiri:Thandizo langa lidzera kuti? Thandizo langa lidzera kwa Yehova,Wakulenga zakumwamba