Masalmo 120:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndinapfuulira kwa Yehova mu msauko wanga,Ndipo anandibvomereza,

2. Yehova, landitsani moyo wanga ku milomo ya mabodza,Ndi ku lilime lonyenga.

3. Adzakuninkhanji, adzakuonjezeranji,Lilime lonyenga iwe?

Masalmo 120