Masalmo 119:81-83 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

81. Moyo wanga unakomoka ndi kukhumba cipulumutso canu:Ndinayembekezera mau anu.

82. Maso anga anatha mphamvu ndi kukhumba mau anu,Ndikuti, Mudzanditonthoza liti?

83. Popeza ndakhala ngati thumba lofukirira;Koma sindiiwala malemba anu.

Masalmo 119