Masalmo 119:32-34 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

32. Ndidzathamangira njira ya malamulo anu,Mutakulitsa mtima wanga.

33. Mundiphunzitse, Yehova, njira ya malemba anu;Ndidzaisunga kufikira kutha kwace.

34. Mundizindikiritse, ndipo ndidzasunga malamulo anu;Ndidzawasamalira ndi mtima wanga wonse.

Masalmo 119