Masalmo 119:112-115 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

112. Ndinalingitsa mtima wanga ucite malemba anu,Kosatha, kufikira cimatiziro.

113. Ndidana nao a mitima iwiri;Koma ndikonda cilamulo canu.

114. Inu ndinu pobisalapo panga, ndi cikopa canga;Ndiyembekezera mau anu.

115. Mundicokere ocita zoipa inu;Kuti ndisunge malamulo a Mulungu wanga.

Masalmo 119