Masalmo 116:10-13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

10. Ndinakhulupirira, cifukwa cace ndinalankhula;Ndinazunzika kwambiri.

11. Pofulumizidwa mtima ndinati ine,Anthu Onse nga mabodza.

12. Ndidzabwezera Yehova cianiCifukwa ca zokoma zace zonse anandicitira?

13. Ndidzanyamula cikho ca cipulumutso,Ndipo ndidzaitanira dzina la Yehova,

Masalmo 116