Masalmo 115:9-13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

9. Israyeli, khulupirira Yehova:Ndiye mthandizi wao ndi cikopa cao.

10. Nyumba ya Aroni, khulupirira Yehova:Ndiye mthandizi wao, ndi cikopa cao.

11. Inu akuopa Yehova, khulupirirani Yehova;Ndiye mthandizi wao ndi cikopa cao.

12. Yehova watikumbukila; adzatidalitsa:Adzadalitsa nyumba ya Israyeli;Adzadalitsa nyumba ya Aroni.

13. Adzadalitsa iwo akuopa Yehova,Ang'ono ndi akuru.

Masalmo 115