Masalmo 115:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92) Kwa ife ai, Yehova, kwa ife ai, Koma kwa dzina lanu patsani ulemerero,Cifukwa ca cifundo canu, ndi coonadi canu.