Masalmo 11:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndakhulupirira Yehova:Mutani nkunena kwa moyo wanga,Thawirani ku phiri lanu ngati mbalame?

2. Pakuti, onani, oipa akoka uta,Apiringidza mubvi wao pansinga,Kuwaponyera mumdima oongoka mtima.

3. Akapasuka maziko,Wolungama angacitenji?

Masalmo 11