Masalmo 109:27-31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

27. Kuti adziwe kuti ici ndi dzanja lanu;Kuti Inu Yehova munacicita.

28. Atemberere iwowa, koma mudalitse ndinu;Pakuuka iwowa adzacita manyazi, koma mtumiki wanu adzakondwera.

29. Otsutsana nane abvale manyazi,Nadzikute naco cisokonezo cao ngati ndi copfunda.

30. Ndidzayamika Yehova kwakukuru pakamwa panga;Ndi pakati pa anthu aunyinji ndidzamlemekeza.

31. Popeza adzaima pa dzanja lamanja la waumphawiKumpulumutsa kwa iwo akuweruza koipa moyo wace.

Masalmo 109