Masalmo 108:11-13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

11. Si ndinu Mulungu, amene mwatitayaOsaturuka nao magulu athu?

12. Tithandizeni mumsauko;Pakuti cipulumutso ca munthu ndi cabe.

13. Mwa Mulungu tidzacita molimbika mtima:Ndipo Iye adzapondereza otisautsa.

Masalmo 108