Masalmo 107:41-43 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

41. Koma aika waumphawi pamsanje posazunzika,Nampatsa mabanja ngati gulu la nkhosa.

42. Oongoka mtima adzaciona nadzasekera;Koma cosalungama conse citseka pakamwa pace.

43. Wokhala nazo nzeru asamalire izi,Ndipo azindikire zacifundo za Yehova,

Masalmo 107