Masalmo 105:4-6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

4. Funani Yehova, ndi mphamvu yace;Funsirani nkhope yace nthawi zonse.

5. Kumbukilani zodabwiza zace adazicita;Zizindikilo zace ndi maweruzo a pakamwa pace;

6. Inu mbeu za Abrahamu, mtumiki wace,Inu ana a Yakobo, osankhika ace.

Masalmo 105