Masalmo 104:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi vinyo wokondweretsa mtima wa munthu,Ndi mafuta akunyezimiritsa nkhope yace,Ndi mkate wakulimbitsa mtima wa munthu.

Masalmo 104

Masalmo 104:5-17