Masalmo 103:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma cifundo ca Yehova ndico coyambira nthawi yosayamba kufikira nthawi yosatha kwa iwo akumuopa Iye,Ndi cilungamo cace kufikira kwa ana a ana;

Masalmo 103

Masalmo 103:15-21