Masalmo 101:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndidzayimba za cifundo ndi ciweruzo;Ndidzayimba zakukulemekezani Inu, Yehova.

2. Ndidzacita mwanzeru m'njira yangwiro;Mudzandidzera liti?Ndidzayenda m'nyumba mwanu ndi mtima wangwiro.

3. Sindidzaika cinthu coipa pamaso panga;Cocita iwo akupatuka padera cindiipira;Sicidzandimamatira.

Masalmo 101