Marko 9:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo panadza mtambo wakuwaphimba iwo; ndipo mau munaturuka m'mtambomo, kuti, Uyu ndiye Mwana wanga wokondedwa; mverani Iye.

Marko 9

Marko 9:1-17