Marko 9:45 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ngati phazi lako likulakwitsa, ulidule; kulowa iwe m'moyo wopunduka mwendo, kuli kwabwino koposa ndi kukhala ndi mapazi ako awiri ndi kuponyedwa m'gehena.[

Marko 9

Marko 9:39-50