Marko 9:38 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Yohane anati kwa Iye, Mphunzitsi, tinaona munthu alikuturutsa ziwanda m'dzina lanu; ndipo tinamletsa, cifukwa sanalikutsata ife.

Marko 9

Marko 9:32-40