Marko 9:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ananena nao, Ndithu ndinena ndi inu kuti, Alipo ena akuimirira pano, amene sadzalawa imfa konse, kufikira akaona Ufumu wa Mulungu utadza ndi mphamvu.

Marko 9

Marko 9:1-11