Marko 8:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo analamulira anthu a khamulo akhale pansi; natenga mikate isanu ndi iwiriyo, nayamika, nanyema, napatsa ophunzira ace, kuti apereke kwa iwo; ndipo anapereka kwa khamulo.

Marko 8

Marko 8:3-16