Marko 8:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anaturuka Yesu, ndi ophunzira ace, nalowa ku midzi ya ku Kaisareya wa Filipi; ndipo panjira anafunsa ophunzira ace, nanena nao, Kodi anthu anena kuti Ine ndine yani?

Marko 8

Marko 8:19-29