Marko 8:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anamgwira dzanja munthu wakhunguyo, naturukira naye kunja kwa mudzi; ndipo atamthira malobvu m'maso mwace, naika manja pa iye, anamfunsa, Uona kanthu kodi?

Marko 8

Marko 8:14-25