Marko 8:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamene ndinawagawira anthu zikwi zisanu mikate isanu ija, munatola mitanga ingati yodzala ndi makombo? Ananena naye, Khumi ndi iwiri.

Marko 8

Marko 8:18-26