Marko 8:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yesu pamene anazindikira, ananena nao, Bwanji mutsutsana cifukwa mulibe mkate? kodi kufikira tsopano simuzindikira, nisimudziwitsa? kodi muli nayo mitima yanu youma?

Marko 8

Marko 8:9-25