Marko 7:36 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anawalamulira kuti asauze munthu, ali yense; koma monga momwe Iye anawalamulitsa momwenso makamaka analalikira kopambana.

Marko 7

Marko 7:31-37