Marko 7:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Iye anauka nacoka kumeneko, nanka ku maiko a ku Turo ndi Sidoni, Ndipo analowa m'nyumba, nafuna kuti asadziwe anthu; ndipo sanakhoza kubisika.

Marko 7

Marko 7:16-28