Marko 7:20-23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

20. Ndipo anati, Coturuka mwa munthu ndico cidetsa munthu.

21. Pakuti m'kati mwace mwa mitima ya anthu, muturuka maganizo oipa, zaciwerewere,

22. zakuba, zakupha, zacigololo, masiriro, zoipa, cinyengo, cinyanso, diso loipa, mwano, kudzikuza, kupusa:

23. zoipa izi zonse zituruka m'kati, nizidetsa munthu.

Marko 7