Marko 6:34 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anaturuka Iye, naona khamu lalikuru la anthu, nagwidwa cifundo ndi iwo, cifukwa anali ngati nkhosa zopanda mbusa; ndipo anayamba kuwaphunzitsa zinthu zambiri.

Marko 6

Marko 6:26-38