Marko 6:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

pakuti Herode anaopa Yohane, podziwa kuti ali munthu wolungama ndi woyera mtima, ndipo anamsunga iye. Ndipo pamene anamva iye anathedwa nzeru, oakondwa kumva iye.

Marko 6

Marko 6:19-29