Marko 6:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mfumu Herode anamva izi; pakuti dzina lace lidamveka; ndipo ananena, kuti, Yohane Mbatizi wauka kwa akufa, ndipo cifukwa cace mphamvu izi zicitacita mwa Iye.

Marko 6

Marko 6:8-17