Marko 5:42-43 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

42. Ndipo pomwepo buthulo linauka, niliyenda; pakuti linali la zaka khumi ndi ziwiri. Ndipo anadabwa pomwepo ndi kudabwa kwakukuru.

43. Ndipo anawalamulira kwambiri kuti asadziwe ici munthu mmodzi, nawauza kuti ampatse iye kudya.

Marko 5