Marko 5:41 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anagwira dzanja lace la mwana, nanena kwa iye, Talita koumi; ndiko kunena posandulika, Buthu, ndinena ndi iwe, Uka.

Marko 5

Marko 5:40-43