Marko 5:33 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma mkaziyo anacita mantha, ndi kunthunthumira, podziwa cimene anamcitira iye, nadza, namgwadira, namuuza coona conse.

Marko 5

Marko 5:29-42