Marko 5:31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ophunzira ace ananena kwa Iye, Muona kuti khamu lirikukanikiza Inu, ndipo munena kodi, Wandikhudza ndani?

Marko 5

Marko 5:30-33