Marko 4:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo zina zinagwa m'nthaka yabwino, ndipo zinapatsa zipatso, ndi kukula ndi kucuruka; ndipo zinabala kupindula makumi atatu, ndi makumi asanundi limodzi, ndi makumi khumi.

Marko 4

Marko 4:4-15