Marko 4:39 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anauka, nadzudzula mphepo, nati kwa nyanja, kuti, Tonthola, khala bata. Ndipo mphepo inaleka, ndipokunagwa bata lalikuru.

Marko 4

Marko 4:29-41