Marko 4:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti kulibe kanthu kobisika, koma kuti kaonetsedwe; kapena kulibe kanthu kanakhala kam'tseri, koma kuti kakaululidwe.

Marko 4

Marko 4:12-27