Marko 3:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Komatu palibe munthu akhoza kulowa m'nvumba ya mwini mphamvu, ndi kufunkha akatundu ace, koma athange wamanga mwini mphamvuyo; ndipo pamenepo adzafunkha za m'nyumba mwace.

Marko 3

Marko 3:25-32