Marko 2:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pomwepo Yesu pozindikira mumtima mwace kuti alikuganizira comweco mwa iwo okha, ananena nao, Muganiza bwanji zinthu izi m'mitima yanu?

Marko 2

Marko 2:1-10