Marko 2:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma adzadza masiku, pamene mkwati adzacotsedwa kwa iwo, ndipo pamenepo adzasala kudya tsiku lomwelo.

Marko 2

Marko 2:12-28