Marko 2:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ananyamuka iye pomwepo, nasenza mphasa, naturuka pamaso pa iwo onse; kotero kuti anadabwa onse, nalemekeza Mulungu, nanena kuti, Zotere sitinaziona ndi kale lonse.

Marko 2

Marko 2:10-14