Marko 16:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

adzatola njoka, ndipo ngakhale akamwa kanthu kakufa nako, sikadzawapweteka; adzaika manja ao pa odwala, ndipo adzacira.

Marko 16

Marko 16:16-20