Marko 15:40 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo analinso kumeneko akazi akuyang'anira kutali; mwa iwo anali Maliya wa Magadala, ndi Maliya amace wa Yakobo wamng'ono ndi wa Yose, ndi Salome;

Marko 15

Marko 15:35-46