Marko 15:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anakangamiza wina wopitirirapo, Simoni wa ku Kurene, alikucokera kuminda, atate wao wa Alesandere ndi Rufu, kuti anyamule mtanda wace.

Marko 15

Marko 15:15-29