Marko 14:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndithu ndinena ndi inu, Ponse pamene padzalalikidwa Uthenga Wabwino ku dziko lonse lapansi, icinso cimene anacita mkazi uyu cidzanenedwa, cikhale comkumbukira naco.

Marko 14

Marko 14:5-11