Marko 14:72 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pomwepo tambala analira kaciwiri. Ndipo Petro anakumbukila umo Yesu anati kwa iye, kuti, Tambala asanalire kawiri udzandikana katatu. Ndipo pakuganizira ici analira misozi.

Marko 14

Marko 14:63-72