Marko 14:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti muli nao aumphawi pamodzi ndi inu masiku onse, ndipo pali ponse pamene mukafuna mukhoza kuwacitira zabwino; koma Ine simuli nane masiku onse.

Marko 14

Marko 14:2-13